tatewachikondi.com
Wolemba Adrian Ebens
Losindikizidwa Epulo 11, 2021
Zokopera 594

Nchifukwa chiyani Mtanda unkafunika ndipo ndani anaufuna?

Nchifukwa chiyani Mtanda unali wofunikira pa chipulumutso chathu?

Kodi mkwiyo wa Mulungu unakwaniritsidwa ndi imfa ya Mwana Wake?

Kodi chilungamo cha Mulungu ndi chiyani ndipo ndi chosiyana ndi chilungamo chathu?

Chifukwa chiyani Yesu adadzifanizira ndi njoka ya mkuwa pa mtengo?

Kodi malo opatulika achi Israeleakutiuza chiyani za Mtanda?